2 Mafumu 21:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Manase+ anali ndi zaka 12 pamene anayamba kulamulira, ndipo analamulira zaka 55 ku Yerusalemu. Mayi ake dzina lawo linali Hefiziba. Mateyu 1:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Hezekiya anabereka Manase.+Manase+ anabereka Amoni.+Amoni+ anabereka Yosiya.
21 Manase+ anali ndi zaka 12 pamene anayamba kulamulira, ndipo analamulira zaka 55 ku Yerusalemu. Mayi ake dzina lawo linali Hefiziba.