Genesis 12:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Iye anatenga mkazi wake Sarai,+ Loti mwana wa m’bale wake,+ ndi chuma chawo chonse,+ komanso akapolo awo onse amene anapeza kudziko la Harana. Iwo ananyamuka ulendo wopita kudziko la Kanani.+ Potsirizira pake anafika ku Kanani.
5 Iye anatenga mkazi wake Sarai,+ Loti mwana wa m’bale wake,+ ndi chuma chawo chonse,+ komanso akapolo awo onse amene anapeza kudziko la Harana. Iwo ananyamuka ulendo wopita kudziko la Kanani.+ Potsirizira pake anafika ku Kanani.