Deuteronomo 12:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 “Yehova Mulungu wako akadzafutukula malire a dziko lako+ monga mmene wakulonjezera,+ ndipo iwe n’kudzanena kuti, ‘Ndikufuna kudya nyama,’ chifukwa walakalaka kudya nyama, nthawi iliyonse imene mtima wako walakalaka kudya nyama uzidzadya.+
20 “Yehova Mulungu wako akadzafutukula malire a dziko lako+ monga mmene wakulonjezera,+ ndipo iwe n’kudzanena kuti, ‘Ndikufuna kudya nyama,’ chifukwa walakalaka kudya nyama, nthawi iliyonse imene mtima wako walakalaka kudya nyama uzidzadya.+