Numeri 26:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Zera amene anali kholo la banja la Azera, ndi Shauli+ amene anali kholo la banja la Ashauli.