2 Mbiri 26:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Wansembe wamkulu Azariya ndi ansembe ena onse atamuyang’ana, anangoona kuti wachita khate pamphumi.+ Choncho anayamba kumutulutsa msangamsanga, ndipo mwiniwakeyonso anatuluka mofulumira chifukwa Yehova anali atamulanga.+
20 Wansembe wamkulu Azariya ndi ansembe ena onse atamuyang’ana, anangoona kuti wachita khate pamphumi.+ Choncho anayamba kumutulutsa msangamsanga, ndipo mwiniwakeyonso anatuluka mofulumira chifukwa Yehova anali atamulanga.+