1 Samueli 1:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Pamene chaka chinkatha, Hana anatenga pakati ndipo anabereka mwana wamwamuna n’kumutcha dzina lake+ Samueli,* chifukwa anati, “ndinam’pempha+ kwa Yehova.” 1 Samueli 8:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndiyeno zimene zinachitika n’zakuti, Samueli atakalamba anaika+ ana ake aamuna kukhala oweruza mu Isiraeli.
20 Pamene chaka chinkatha, Hana anatenga pakati ndipo anabereka mwana wamwamuna n’kumutcha dzina lake+ Samueli,* chifukwa anati, “ndinam’pempha+ kwa Yehova.”
8 Ndiyeno zimene zinachitika n’zakuti, Samueli atakalamba anaika+ ana ake aamuna kukhala oweruza mu Isiraeli.