Yoswa 19:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Maere+ achiwiri anagwera Simiyoni, kapena kuti fuko la ana a Simiyoni,+ potsata mabanja awo. Cholowa chawo chinali pakati pa cholowa cha ana a Yuda.+
19 Maere+ achiwiri anagwera Simiyoni, kapena kuti fuko la ana a Simiyoni,+ potsata mabanja awo. Cholowa chawo chinali pakati pa cholowa cha ana a Yuda.+