Yoswa 21:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Mabanja a ana a Kohati, kapena kuti Alevi otsala pa ana a Kohati, anapatsidwa mizinda yochokera m’fuko la Efuraimu. Iwo anapatsidwa mizindayi pambuyo pochita maere.+
20 Mabanja a ana a Kohati, kapena kuti Alevi otsala pa ana a Kohati, anapatsidwa mizinda yochokera m’fuko la Efuraimu. Iwo anapatsidwa mizindayi pambuyo pochita maere.+