Yoswa 19:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Anapitirira mpaka ku Eburoni, Rehobu, Hamoni, Kana, mpaka kumzinda wa anthu ambiri wa Sidoni.+ Oweruza 1:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Fuko la Aseri+ silinapitikitse anthu okhala mumzinda wa Ako ndi anthu okhala m’mizinda ya Sidoni,+ Alabu, Akizibu,+ Heliba, Afiki+ ndi Rehobu.+
31 Fuko la Aseri+ silinapitikitse anthu okhala mumzinda wa Ako ndi anthu okhala m’mizinda ya Sidoni,+ Alabu, Akizibu,+ Heliba, Afiki+ ndi Rehobu.+