Yoswa 19:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Kuchokera kumeneko, malirewo analowera chakum’mawa n’kukafika ku Gati-heferi,+ ku Eti-kazini, ndi ku Rimoni, mpaka ku Nea. Yoswa 21:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Dimena+ ndi malo ake odyetserako ziweto, ndiponso Nahalala+ ndi malo ake odyetserako ziweto. Yonse pamodzi inalipo mizinda inayi.
13 Kuchokera kumeneko, malirewo analowera chakum’mawa n’kukafika ku Gati-heferi,+ ku Eti-kazini, ndi ku Rimoni, mpaka ku Nea.
35 Dimena+ ndi malo ake odyetserako ziweto, ndiponso Nahalala+ ndi malo ake odyetserako ziweto. Yonse pamodzi inalipo mizinda inayi.