Aheberi 11:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Mwa chikhulupiriro, Inoki+ anasamutsidwa kuti asafe mozunzika, moti sanapezeke kwina kulikonse chifukwa Mulungu anamusamutsa.+ Pakuti asanasamutsidwe, Mulungu anamuchitira umboni kuti akukondwera naye.+ Yuda 14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ngakhalenso Inoki,+ wa m’badwo wa 7 kuchokera kwa Adamu, analosera za iwowa pamene anati: “Taonani! Yehova anabwera ndi miyandamiyanda ya oyera ake,*+
5 Mwa chikhulupiriro, Inoki+ anasamutsidwa kuti asafe mozunzika, moti sanapezeke kwina kulikonse chifukwa Mulungu anamusamutsa.+ Pakuti asanasamutsidwe, Mulungu anamuchitira umboni kuti akukondwera naye.+
14 Ngakhalenso Inoki,+ wa m’badwo wa 7 kuchokera kwa Adamu, analosera za iwowa pamene anati: “Taonani! Yehova anabwera ndi miyandamiyanda ya oyera ake,*+