Genesis 50:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Kenako anafika pamalo opunthira mbewu+ a Atadi m’chigawo cha Yorodano.+ Kumeneko, anthuwo analira ndi kubuma kwakukulu, ndipo Yosefe anachita nawo miyambo yolirira maliro a bambo ake kwa masiku 7.+ 2 Samueli 3:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Pambuyo pake, anthu onse anabwera kwa Davide tsiku lomwelo kudzam’patsa chakudya+ chomutonthoza, koma Davide analumbira kuti: “Mulungu andilange+ mowirikiza ngati ndidzalawa chakudya kapena kena kalikonse dzuwa lisanalowe!”+
10 Kenako anafika pamalo opunthira mbewu+ a Atadi m’chigawo cha Yorodano.+ Kumeneko, anthuwo analira ndi kubuma kwakukulu, ndipo Yosefe anachita nawo miyambo yolirira maliro a bambo ake kwa masiku 7.+
35 Pambuyo pake, anthu onse anabwera kwa Davide tsiku lomwelo kudzam’patsa chakudya+ chomutonthoza, koma Davide analumbira kuti: “Mulungu andilange+ mowirikiza ngati ndidzalawa chakudya kapena kena kalikonse dzuwa lisanalowe!”+