Genesis 16:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Mngelo wa Yehovayo anapitiriza kulankhula ndi mkaziyo kuti: “Taona, panopo uli ndi pakati, ndipo udzabereka mwana wamwamuna. Mwanayo udzamutche Isimaeli,+ pakuti Yehova wamva kulira kwako.+
11 Mngelo wa Yehovayo anapitiriza kulankhula ndi mkaziyo kuti: “Taona, panopo uli ndi pakati, ndipo udzabereka mwana wamwamuna. Mwanayo udzamutche Isimaeli,+ pakuti Yehova wamva kulira kwako.+