Oweruza 19:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Anauzanso mtumiki wakeyo kuti: “Tiyeni tifike pa amodzi mwa malo awa, Gibeya kapena Rama,+ ndipo tigone kumeneko.”
13 Anauzanso mtumiki wakeyo kuti: “Tiyeni tifike pa amodzi mwa malo awa, Gibeya kapena Rama,+ ndipo tigone kumeneko.”