Genesis 25:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ana a Midiyani anali Efa,+ Eferi, Hanoki, Abida ndi Elida.+ Onsewa anali ana aamuna a Ketura.