Yeremiya 2:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Tamverani mawu a Yehova, inu a m’nyumba ya Yakobo+ ndi inu nonse mafuko a m’nyumba ya Isiraeli.+