1 Mafumu 22:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Ndiyeno mfumu ya Isiraeli inati: “Tengani Mikaya mubwerere naye kwa Amoni mkulu wa mzinda, ndi kwa Yowasi mwana wa mfumu.+
26 Ndiyeno mfumu ya Isiraeli inati: “Tengani Mikaya mubwerere naye kwa Amoni mkulu wa mzinda, ndi kwa Yowasi mwana wa mfumu.+