1 Mafumu 6:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Makoma a mkati mwa nyumbayo anawamanga ndi matabwa akuluakulu a mkungudza. Mkati mwa nyumbayo, kuchokera pansi mpaka kudenga* anakutamo ndi matabwa. Kenako anakuta pansi pa nyumbayo ndi matabwa akuluakulu a mitengo yofanana ndi mkungudza.+
15 Makoma a mkati mwa nyumbayo anawamanga ndi matabwa akuluakulu a mkungudza. Mkati mwa nyumbayo, kuchokera pansi mpaka kudenga* anakutamo ndi matabwa. Kenako anakuta pansi pa nyumbayo ndi matabwa akuluakulu a mitengo yofanana ndi mkungudza.+