2 Mbiri 6:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Tsopano Solomo anaimirira patsogolo pa guwa lansembe la Yehova patsogolo pa mpingo wonse wa Isiraeli.+ Kenako anatambasula manja ake.+ 2 Mbiri 7:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Tsopano maso anga+ akhala otseguka ndipo makutu anga+ azimvetsera mapemphero onenedwa pamalo ano.
12 Tsopano Solomo anaimirira patsogolo pa guwa lansembe la Yehova patsogolo pa mpingo wonse wa Isiraeli.+ Kenako anatambasula manja ake.+