1 Mafumu 6:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Solomo anakuta+ mkati mwa nyumba yonseyo ndi golide woyenga bwino.+ Anatenga matcheni+ agolide ndi kuwadutsitsa kutsogolo kwa chipinda chamkati,+ n’kukuta chipindacho ndi golide.
21 Solomo anakuta+ mkati mwa nyumba yonseyo ndi golide woyenga bwino.+ Anatenga matcheni+ agolide ndi kuwadutsitsa kutsogolo kwa chipinda chamkati,+ n’kukuta chipindacho ndi golide.