2 Mafumu 8:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Yehoramu anakhala mfumu ali ndi zaka 32, ndipo analamulira ku Yerusalemu zaka 8.+