-
1 Samueli 30:3Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
3 Davide atafika mumzindawo pamodzi ndi amuna amene anali kuyenda naye, anangoona kuti mzindawo watenthedwa ndi moto ndipo akazi awo, ana awo aamuna ndi ana awo aakazi agwidwa ndi kutengedwa.
-