1 Mbiri 9:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Abale awo amene anali kukhala m’midzi yawo, ankabwera nthawi ndi nthawi kudzagwira ntchito limodzi nawo kwa masiku 7.+ Luka 1:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Tsopano pamene Zekariya anali kugwira ntchito monga wansembe pamaso pa Mulungu, kuimira gawo lake,+
25 Abale awo amene anali kukhala m’midzi yawo, ankabwera nthawi ndi nthawi kudzagwira ntchito limodzi nawo kwa masiku 7.+
8 Tsopano pamene Zekariya anali kugwira ntchito monga wansembe pamaso pa Mulungu, kuimira gawo lake,+