2 Mafumu 11:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Atsogoleri a magulu a asilikali 100+ anachita mogwirizana ndi zonse zimene wansembe Yehoyada analamula. Choncho, aliyense anatenga amuna ake amene anali kulowa pa sabata,+ pamodzi ndi amene anali kutuluka pa sabata, n’kupita kwa wansembe Yehoyada.
9 Atsogoleri a magulu a asilikali 100+ anachita mogwirizana ndi zonse zimene wansembe Yehoyada analamula. Choncho, aliyense anatenga amuna ake amene anali kulowa pa sabata,+ pamodzi ndi amene anali kutuluka pa sabata, n’kupita kwa wansembe Yehoyada.