2 Mafumu 11:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Choncho anamugwira n’kumutulutsira pakhomo la kunyumba ya mfumu+ lolowera mahatchi,+ ndipo anam’phera pamenepo.+
16 Choncho anamugwira n’kumutulutsira pakhomo la kunyumba ya mfumu+ lolowera mahatchi,+ ndipo anam’phera pamenepo.+