2 Mafumu 12:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 wansembe aliyense atenge ndalama zimenezi kwa anthu owadziwa,+ ndipo anthuwo kumbali yawo akonze ming’alu ya nyumbayo paliponse pamene pali mng’alu.”+
5 wansembe aliyense atenge ndalama zimenezi kwa anthu owadziwa,+ ndipo anthuwo kumbali yawo akonze ming’alu ya nyumbayo paliponse pamene pali mng’alu.”+