2 Mafumu 12:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Chotero Mfumu Yehoasi+ anaitana wansembe Yehoyada ndi ansembe ena n’kuwafunsa kuti: “N’chifukwa chiyani simukukonza ming’alu ya nyumbayi? Tsopano musatengenso ndalama zina kwa anthu owadziwa, koma muzipereke kuti akonzere ming’alu ya nyumbayi.”+
7 Chotero Mfumu Yehoasi+ anaitana wansembe Yehoyada ndi ansembe ena n’kuwafunsa kuti: “N’chifukwa chiyani simukukonza ming’alu ya nyumbayi? Tsopano musatengenso ndalama zina kwa anthu owadziwa, koma muzipereke kuti akonzere ming’alu ya nyumbayi.”+