Nehemiya 10:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Kuwonjezera apo, tinadziikira malamulo akuti chaka chilichonse aliyense wa ife azipereka gawo limodzi mwa magawo atatu a sekeli kuti ndalama zimenezo akazigwiritsire ntchito pa utumiki wa panyumba ya Mulungu wathu.+ Mateyu 17:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Atafika ku Kaperenao, anthu okhometsa msonkho wa madalakima awiri anafikira Petulo ndi kumufunsa kuti: “Kodi mphunzitsi wanu amapereka madalakima awiri a msonkho?”+
32 Kuwonjezera apo, tinadziikira malamulo akuti chaka chilichonse aliyense wa ife azipereka gawo limodzi mwa magawo atatu a sekeli kuti ndalama zimenezo akazigwiritsire ntchito pa utumiki wa panyumba ya Mulungu wathu.+
24 Atafika ku Kaperenao, anthu okhometsa msonkho wa madalakima awiri anafikira Petulo ndi kumufunsa kuti: “Kodi mphunzitsi wanu amapereka madalakima awiri a msonkho?”+