2 Mafumu 12:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Akangoona kuti m’bokosilo muli ndalama zambiri, mlembi+ wa mfumu ndi mkulu wa ansembe ankabwera n’kuwerenga ndi kumanga pamodzi ndalama zimene zinali kupezeka panyumba ya Yehova.+
10 Akangoona kuti m’bokosilo muli ndalama zambiri, mlembi+ wa mfumu ndi mkulu wa ansembe ankabwera n’kuwerenga ndi kumanga pamodzi ndalama zimene zinali kupezeka panyumba ya Yehova.+