11 Anthu ogwira ntchitowa anapereka ndalamazo kwa amisiri ndi kwa omanga+ nyumba kuti agulire miyala yosema+ ndi matabwa opangira zida zomangira zinthu pamodzi, ndiponso kuti akhome mitanda m’nyumba zimene mafumu+ a Yuda anazilekerera kuti ziwonongeke.