Ekisodo 37:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Atatero anapanga ziwiya za patebulolo, mbale zake, zikho zake, mitsuko yake ndi mbale zake zolowa zoti azithirira nsembe zachakumwa. Anazipanga ndi golide woyenga bwino.+ Numeri 7:84 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 84 Potsegulira guwa lansembe,+ pa tsiku limene guwalo linadzozedwa, atsogoleri+ a Isiraeli anapereka izi: Mbale zikuluzikulu zasiliva 12, mbale zolowa zasiliva+ 12, zikho zagolide 12.
16 Atatero anapanga ziwiya za patebulolo, mbale zake, zikho zake, mitsuko yake ndi mbale zake zolowa zoti azithirira nsembe zachakumwa. Anazipanga ndi golide woyenga bwino.+
84 Potsegulira guwa lansembe,+ pa tsiku limene guwalo linadzozedwa, atsogoleri+ a Isiraeli anapereka izi: Mbale zikuluzikulu zasiliva 12, mbale zolowa zasiliva+ 12, zikho zagolide 12.