2 Mbiri 4:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Anapanganso maluwa agolide, nyale zagolide, zopanira+ zagolide zozimitsira nyale, (golide wake anali woyengedwa bwino kwambiri,) 2 Mbiri 4:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 zozimitsira nyale, mbale zolowa, makapu, ndi zopalira moto. Zonsezi zinali zagolide woyenga bwino.+ Anapanganso khomo lolowera m’nyumbayo,+ zitseko zamkati za Chipinda Choyera Koposa, ndi zitseko+ za nyumbayo. Zonsezi zinali zagolide.
21 Anapanganso maluwa agolide, nyale zagolide, zopanira+ zagolide zozimitsira nyale, (golide wake anali woyengedwa bwino kwambiri,)
22 zozimitsira nyale, mbale zolowa, makapu, ndi zopalira moto. Zonsezi zinali zagolide woyenga bwino.+ Anapanganso khomo lolowera m’nyumbayo,+ zitseko zamkati za Chipinda Choyera Koposa, ndi zitseko+ za nyumbayo. Zonsezi zinali zagolide.