2 Mafumu 12:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Atumiki ake amene anamupha anali Yozakara+ mwana wa Simeyati ndi Yehozabadi mwana wa Someri. Choncho anamuika m’manda mu Mzinda wa Davide pamodzi ndi makolo ake, ndipo Amaziya+ mwana wake anayamba kulamulira m’malo mwake.
21 Atumiki ake amene anamupha anali Yozakara+ mwana wa Simeyati ndi Yehozabadi mwana wa Someri. Choncho anamuika m’manda mu Mzinda wa Davide pamodzi ndi makolo ake, ndipo Amaziya+ mwana wake anayamba kulamulira m’malo mwake.