2 Mbiri 17:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Kuchokera m’fuko la Benjamini+ panali Eliyada, mwamuna wamphamvu ndi wolimba mtima yemwe anali ndi asilikali 200,000 onyamula mauta ndi zishango.+
17 Kuchokera m’fuko la Benjamini+ panali Eliyada, mwamuna wamphamvu ndi wolimba mtima yemwe anali ndi asilikali 200,000 onyamula mauta ndi zishango.+