-
1 Samueli 17:38Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
38 Tsopano Sauli anayamba kuveka Davide zovala zake. Anamuveka chisoti chamkuwa kumutu kwake, komanso chovala chamamba achitsulo.
-