Numeri 12:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Kenako mtambo uja unachoka pamwamba pa chihemacho. Pomwepo, Miriamu anagwidwa ndi khate loyera mbuu!+ Aroni atacheuka, anangoona kuti Miriamu wachita khate.+ 2 Mafumu 5:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Tsopano khate+ la Namani limamatira iweyo ndi mbadwa zako mpaka kalekale.”*+ Nthawi yomweyo Gehazi anachoka pamaso pa Elisa, atachita khate loyera kuti mbuu.+
10 Kenako mtambo uja unachoka pamwamba pa chihemacho. Pomwepo, Miriamu anagwidwa ndi khate loyera mbuu!+ Aroni atacheuka, anangoona kuti Miriamu wachita khate.+
27 Tsopano khate+ la Namani limamatira iweyo ndi mbadwa zako mpaka kalekale.”*+ Nthawi yomweyo Gehazi anachoka pamaso pa Elisa, atachita khate loyera kuti mbuu.+