2 Mafumu 16:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ahazi ankafukiza ndi kupereka nsembe yautsi pamalo okwezeka,+ pamapiri,+ ndi pansi pa mtengo uliwonse waukulu wa masamba obiriwira.+
4 Ahazi ankafukiza ndi kupereka nsembe yautsi pamalo okwezeka,+ pamapiri,+ ndi pansi pa mtengo uliwonse waukulu wa masamba obiriwira.+