Luka 6:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 “Koma inu amene mukumvetseranu ine ndikukuuzani kuti, Pitirizani kukonda adani anu+ ndi kuchita zabwino+ kwa amene akudana nanu. Aroma 12:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Koma “ngati mdani wako ali ndi njala, um’patse chakudya. Ngati ali ndi ludzu, um’patse chakumwa.+ Pakuti mwa kutero udzamuunjikira makala a moto pamutu pake.”+
27 “Koma inu amene mukumvetseranu ine ndikukuuzani kuti, Pitirizani kukonda adani anu+ ndi kuchita zabwino+ kwa amene akudana nanu.
20 Koma “ngati mdani wako ali ndi njala, um’patse chakudya. Ngati ali ndi ludzu, um’patse chakumwa.+ Pakuti mwa kutero udzamuunjikira makala a moto pamutu pake.”+