Aroma 15:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Ife olimba tiyenera kunyamula zofooka za osalimba,+ osati kumadzikondweretsa tokha ayi.+