Numeri 22:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Kenako, ana a Isiraeli anasamuka kumaloko n’kukamanga msasa m’chipululu cha Mowabu,+ moyang’anana ndi Yeriko patsidya pa mtsinje wa Yorodano. Yoswa 6:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Mzinda wa Yeriko unatsekedwa mwamphamvu chifukwa cha ana a Isiraeli. Palibe amene anali kutuluka kapena kulowa mumzindawo.+
22 Kenako, ana a Isiraeli anasamuka kumaloko n’kukamanga msasa m’chipululu cha Mowabu,+ moyang’anana ndi Yeriko patsidya pa mtsinje wa Yorodano.
6 Mzinda wa Yeriko unatsekedwa mwamphamvu chifukwa cha ana a Isiraeli. Palibe amene anali kutuluka kapena kulowa mumzindawo.+