Oweruza 14:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Tsopano Samisoni anapita ku Timuna+ ndipo kumeneko anaona mkazi mwa ana aakazi a Afilisiti.