Levitiko 4:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 “‘Tsopano ngati khamu lonse la Isiraeli lachita cholakwa,+ mwa kuchita chimodzi mwa zinthu zimene Yehova analamula kuti asachite ndipo chawapalamulitsa, koma mpingo wonse sunazindikire kuti walakwa,+
13 “‘Tsopano ngati khamu lonse la Isiraeli lachita cholakwa,+ mwa kuchita chimodzi mwa zinthu zimene Yehova analamula kuti asachite ndipo chawapalamulitsa, koma mpingo wonse sunazindikire kuti walakwa,+