2 Mbiri 12:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Akalonga a Isiraeliwo ndi mfumuyo atamva zimenezi, anadzichepetsa+ n’kunena kuti: “Yehova ndi wolungama.”+
6 Akalonga a Isiraeliwo ndi mfumuyo atamva zimenezi, anadzichepetsa+ n’kunena kuti: “Yehova ndi wolungama.”+