Numeri 9:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 “Uza ana a Isiraeli kuti, ‘Munthu wina aliyense mwa inu kapena mwa mbadwa zanu, amene wadetsedwa pokhudza mtembo wa munthu,+ kapena amene ali pa ulendo wautali, akonzebe nsembe ya pasika yopereka kwa Yehova.
10 “Uza ana a Isiraeli kuti, ‘Munthu wina aliyense mwa inu kapena mwa mbadwa zanu, amene wadetsedwa pokhudza mtembo wa munthu,+ kapena amene ali pa ulendo wautali, akonzebe nsembe ya pasika yopereka kwa Yehova.