12 Panalinso mapulani a kamangidwe ka zonse zimene anauzidwa kudzera mwa mzimu+ zokhudza mabwalo+ a nyumba ya Yehova, zipinda zonse zodyeramo+ kuzungulira kachisi, chuma cha nyumba ya Mulungu woona, ndi chuma cha zinthu zimene anaziyeretsa kukhala zopatulika.+