Levitiko 19:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 “‘Musadye chilichonse limodzi ndi magazi.+ “‘Musaombeze*+ ndipo musachite zamatsenga.+