2 Mbiri 29:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Atatero analowa kumene kunali mfumu Hezekiya n’kukaiuza kuti: “Tayeretsa nyumba yonse ya Yehova, guwa lansembe+ zopsereza ndi ziwiya zake zonse,+ ndiponso tebulo+ loikapo mkate wosanjikiza ndi ziwiya zake zonse.+
18 Atatero analowa kumene kunali mfumu Hezekiya n’kukaiuza kuti: “Tayeretsa nyumba yonse ya Yehova, guwa lansembe+ zopsereza ndi ziwiya zake zonse,+ ndiponso tebulo+ loikapo mkate wosanjikiza ndi ziwiya zake zonse.+