2 Mafumu 21:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Chotero anamuika m’manda ake m’munda wa Uziza,+ ndipo Yosiya+ mwana wake anayamba kulamulira m’malo mwake.
26 Chotero anamuika m’manda ake m’munda wa Uziza,+ ndipo Yosiya+ mwana wake anayamba kulamulira m’malo mwake.