Levitiko 10:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Kutinso muziphunzitsa ana a Isiraeli+ malamulo onse amene Yehova wanena kwa iwo kudzera mwa Mose.” Levitiko 26:46 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 46 Amenewa ndiwo malangizo, zigamulo+ ndi malamulo amene Yehova anaika pakati pa iye ndi ana a Isiraeli m’phiri la Sinai, kudzera mwa Mose.+
11 Kutinso muziphunzitsa ana a Isiraeli+ malamulo onse amene Yehova wanena kwa iwo kudzera mwa Mose.”
46 Amenewa ndiwo malangizo, zigamulo+ ndi malamulo amene Yehova anaika pakati pa iye ndi ana a Isiraeli m’phiri la Sinai, kudzera mwa Mose.+