1 Mbiri 16:37 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 Kenako Davide anasiya Asafu+ ndi abale ake kumeneko pamaso pa likasa la Yehova, kuti azitumikira+ pamaso pa Likasalo nthawi zonse, malinga ndi zofunikira pa tsiku lililonse.+ 2 Mbiri 29:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Kuchokera mwa ana a Elizafana+ panali Simuri ndi Yeweli. Kuchokera mwa ana a Asafu+ panali Zekariya ndi Mataniya. Salimo 50:kam Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika Nyimbo ya Asafu.+
37 Kenako Davide anasiya Asafu+ ndi abale ake kumeneko pamaso pa likasa la Yehova, kuti azitumikira+ pamaso pa Likasalo nthawi zonse, malinga ndi zofunikira pa tsiku lililonse.+
13 Kuchokera mwa ana a Elizafana+ panali Simuri ndi Yeweli. Kuchokera mwa ana a Asafu+ panali Zekariya ndi Mataniya.